1 Samueli 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musapatuke kuti mutsatire milungu yopanda pake,+ yopanda phindu,+ imene singakulanditseni, pakuti ndi yopanda pake. Habakuku 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi chifaniziro chosema, chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndiponso mphunzitsi wonama,+ zili ndi phindu lanji+ kuti wozipanga azizikhulupirira+ ndipo azipanga milungu yopanda pake yosalankhula?+
21 Musapatuke kuti mutsatire milungu yopanda pake,+ yopanda phindu,+ imene singakulanditseni, pakuti ndi yopanda pake.
18 Kodi chifaniziro chosema, chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndiponso mphunzitsi wonama,+ zili ndi phindu lanji+ kuti wozipanga azizikhulupirira+ ndipo azipanga milungu yopanda pake yosalankhula?+