Yeremiya 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Yehova wanena kuti: “Tsopano ndikuikira anthu awa zinthu zopunthwitsa,+ ndipo onse pamodzi, abambo ndi ana, adzapunthwa pa zinthu zimenezi, munthu aliyense limodzi ndi mnzake adzatheratu.”+ Ezekieli 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘“Choncho pakati pako, abambo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumphepo zonse zinayi.”’+ Mateyu 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso munthu adzapereka m’bale+ wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake. Ana adzaukira makolo awo ndipo adzawaphetsa.+
21 Choncho Yehova wanena kuti: “Tsopano ndikuikira anthu awa zinthu zopunthwitsa,+ ndipo onse pamodzi, abambo ndi ana, adzapunthwa pa zinthu zimenezi, munthu aliyense limodzi ndi mnzake adzatheratu.”+
10 “‘“Choncho pakati pako, abambo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumphepo zonse zinayi.”’+
21 Komanso munthu adzapereka m’bale+ wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake. Ana adzaukira makolo awo ndipo adzawaphetsa.+