Maliro 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Khungu lathu latentha kwambiri ngati ng’anjo, chifukwa cha njala yaikulu.+