2 Mafumu 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala+ inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+ Yobu 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Khungu langa linakhala lakuda+ ndipo linayoyoka pathupi panga.Mafupa anga anatentha chifukwa chouma. Maliro 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala. Anthu sakuwazindikiranso mumsewu.+Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo.
3 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala+ inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+
30 Khungu langa linakhala lakuda+ ndipo linayoyoka pathupi panga.Mafupa anga anatentha chifukwa chouma.
8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala. Anthu sakuwazindikiranso mumsewu.+Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo.