Salimo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu ameneyo adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa mitsinje ya madzi,+Umene umabala zipatso m’nyengo yake,+Umenenso masamba ake safota,+Ndipo zochita zake zonse zidzamuyendera bwino.+ Salimo 92:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wolungama adzakula ngati mtengo wa kanjedza,+Ndipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+
3 Munthu ameneyo adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa mitsinje ya madzi,+Umene umabala zipatso m’nyengo yake,+Umenenso masamba ake safota,+Ndipo zochita zake zonse zidzamuyendera bwino.+
12 Wolungama adzakula ngati mtengo wa kanjedza,+Ndipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+