Yeremiya 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Hema wanga wafunkhidwa, ndipo zingwe zanga zonse zomangira hemayo aziduladula.+ Ana anga aamuna achoka ndi kundisiya ndipo kulibenso.+ Komanso palibe wotambasula kapena kudzutsa hema wanga.
20 Hema wanga wafunkhidwa, ndipo zingwe zanga zonse zomangira hemayo aziduladula.+ Ana anga aamuna achoka ndi kundisiya ndipo kulibenso.+ Komanso palibe wotambasula kapena kudzutsa hema wanga.