Yeremiya 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Alengeza za kuphwanya kosakaziratu pakuti dziko lonse lafunkhidwa.+ Mwadzidzidzi, mahema anga ndi nsalu za mahema angawo zafunkhidwa+ m’kanthawi kochepa. Maliro 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wakunga uta wake ngati mdani.+ Dzanja lake lamanja+ lakonzeka ngati la mdani,+Ndipo wapitiriza kupha+ anthu onse ofunika kwambiri.Ukali wake waukhuthula ngati moto+ m’hema+ wa mwana wamkazi wa Ziyoni.
20 Alengeza za kuphwanya kosakaziratu pakuti dziko lonse lafunkhidwa.+ Mwadzidzidzi, mahema anga ndi nsalu za mahema angawo zafunkhidwa+ m’kanthawi kochepa.
4 Wakunga uta wake ngati mdani.+ Dzanja lake lamanja+ lakonzeka ngati la mdani,+Ndipo wapitiriza kupha+ anthu onse ofunika kwambiri.Ukali wake waukhuthula ngati moto+ m’hema+ wa mwana wamkazi wa Ziyoni.