Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Pakuti mivi ya Wamphamvuyonse yandilasa,+

      Ndipo ine ndikumwa poizoni wa miviyo.+

      Zoopsa zochokera kwa Mulungu zasonkhana kuti zilimbane nane.+

  • Yesaya 63:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma iwo anapanduka+ ndi kukhumudwitsa mzimu wake woyera.+ Chotero iye anasintha n’kukhala mdani+ wawo ndipo anachita nawo nkhondo.+

  • Yeremiya 21:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima, ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+

  • Yeremiya 30:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Achigololo onse amene anali kukukonda kwambiri akuiwala.+ Iwo sakukufunafunanso. Ndakumenya ndi mkwapulo+ ngati mdani ndipo ndakulanga ngati munthu wankhanza+ chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zako.+ Machimo ako achuluka kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena