Salimo 88:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 88 Inu Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa,+Masana ndimafuula kwa inu,+Usikunso ndimafuula pamaso panu.+ Danieli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+
88 Inu Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa,+Masana ndimafuula kwa inu,+Usikunso ndimafuula pamaso panu.+
3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+