Yobu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mutu wanga ukadzikweza,+ mudzandisaka ngati kuti ndinu mkango wamphamvu,+Ndipo mudzandichitira chinthu chinanso chodabwitsa. Yobu 38:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ikamyata m’malo amene imabisala,+Kapena ikabisala patchire kuti igwire nyama? Hoseya 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndidzakhala ngati mkango wamphamvu kwa Efuraimu+ ndiponso ngati mkango wamphongo kwa nyumba ya Yuda. Ineyo ndidzawakhadzulakhadzula ndekha ndi kuwataya ndipo sipadzakhala wowalanditsa.+
16 Mutu wanga ukadzikweza,+ mudzandisaka ngati kuti ndinu mkango wamphamvu,+Ndipo mudzandichitira chinthu chinanso chodabwitsa.
14 Ine ndidzakhala ngati mkango wamphamvu kwa Efuraimu+ ndiponso ngati mkango wamphongo kwa nyumba ya Yuda. Ineyo ndidzawakhadzulakhadzula ndekha ndi kuwataya ndipo sipadzakhala wowalanditsa.+