Salimo 50:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+ Maliro 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kwa ine, iye ali ngati chimbalangondo chimene chandibisalira,+ ndiponso ngati mkango umene wakhala pamalo obisika.+
22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+
10 Kwa ine, iye ali ngati chimbalangondo chimene chandibisalira,+ ndiponso ngati mkango umene wakhala pamalo obisika.+