Hoseya 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzawaukira ngati chimbalangondo chimene ana ake asowa+ ndipo ndidzang’amba zifuwa zawo, mmene muli mitima yawo. Ndidzawadya kumeneko ngati mkango.+ Chilombo chakuthengo chidzawakhadzulakhadzula.+ Amosi 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 monga mmene zingakhalire kuti munthu pothawa mkango akukumana ndi chimbalangondo, ndipo pamene akulowa m’nyumba ndi kugwira khoma njoka ikumuluma.+
8 Ndidzawaukira ngati chimbalangondo chimene ana ake asowa+ ndipo ndidzang’amba zifuwa zawo, mmene muli mitima yawo. Ndidzawadya kumeneko ngati mkango.+ Chilombo chakuthengo chidzawakhadzulakhadzula.+
19 monga mmene zingakhalire kuti munthu pothawa mkango akukumana ndi chimbalangondo, ndipo pamene akulowa m’nyumba ndi kugwira khoma njoka ikumuluma.+