Yobu 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero, kodi chiyembekezo changa chili kuti?+Kodi pali amene akuona kuti ine ndili ndi chiyembekezo? Salimo 31:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma ine nditapanikizika ndinati:+“Ndidzafafanizidwa kuchoka pamaso panu.”+Ndithudi mwamva kuchonderera kwanga pamene ndinali kufuulira kwa inu kupempha thandizo.+
15 Chotero, kodi chiyembekezo changa chili kuti?+Kodi pali amene akuona kuti ine ndili ndi chiyembekezo?
22 Koma ine nditapanikizika ndinati:+“Ndidzafafanizidwa kuchoka pamaso panu.”+Ndithudi mwamva kuchonderera kwanga pamene ndinali kufuulira kwa inu kupempha thandizo.+