Yeremiya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndidzadyetsa anthu amenewa chitsamba chowawa,+ ndipo ndidzawamwetsa madzi apoizoni.+ Maliro 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wandimangira mpanda+ kuti chomera chakupha+ ndi mavuto zindizungulire.
15 Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndidzadyetsa anthu amenewa chitsamba chowawa,+ ndipo ndidzawamwetsa madzi apoizoni.+