Yeremiya 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yehova wa makamu wadzudzula aneneriwo kuti: “Ndiwadyetsa chitsamba chowawa ndipo ndiwamwetsa madzi apoizoni.+ Chifukwa kuchokera mwa aneneri a ku Yerusalemu mpatuko+ wafalikira m’dziko lonse.” Maliro 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Wandipatsa zinthu zowawa zokwanira.+ Wandikhutitsa chitsamba chowawa.+
15 Choncho Yehova wa makamu wadzudzula aneneriwo kuti: “Ndiwadyetsa chitsamba chowawa ndipo ndiwamwetsa madzi apoizoni.+ Chifukwa kuchokera mwa aneneri a ku Yerusalemu mpatuko+ wafalikira m’dziko lonse.”