Yeremiya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndidzadyetsa anthu amenewa chitsamba chowawa,+ ndipo ndidzawamwetsa madzi apoizoni.+ Yeremiya 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yehova wa makamu wadzudzula aneneriwo kuti: “Ndiwadyetsa chitsamba chowawa ndipo ndiwamwetsa madzi apoizoni.+ Chifukwa kuchokera mwa aneneri a ku Yerusalemu mpatuko+ wafalikira m’dziko lonse.”
15 Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndidzadyetsa anthu amenewa chitsamba chowawa,+ ndipo ndidzawamwetsa madzi apoizoni.+
15 Choncho Yehova wa makamu wadzudzula aneneriwo kuti: “Ndiwadyetsa chitsamba chowawa ndipo ndiwamwetsa madzi apoizoni.+ Chifukwa kuchokera mwa aneneri a ku Yerusalemu mpatuko+ wafalikira m’dziko lonse.”