Salimo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngati mwakwiya, musachimwe.+Lankhulani mumtima mwanu, muli pabedi panu,+ ndipo mukhale chete. [Seʹlah.] Maliro 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akuluakulu a mwana wamkazi wa Ziyoni akhala pansi ndipo akhala chete.+Iwo athira fumbi pamitu+ yawo ndipo avala ziguduli.*+Anamwali a Yerusalemu aweramitsa mitu yawo mpaka padothi.+
4 Ngati mwakwiya, musachimwe.+Lankhulani mumtima mwanu, muli pabedi panu,+ ndipo mukhale chete. [Seʹlah.]
10 Akuluakulu a mwana wamkazi wa Ziyoni akhala pansi ndipo akhala chete.+Iwo athira fumbi pamitu+ yawo ndipo avala ziguduli.*+Anamwali a Yerusalemu aweramitsa mitu yawo mpaka padothi.+