Salimo 39:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinakhala chete.+ Sindinatsegule pakamwa panga,+Pakuti inu munachitapo kanthu.+ Yeremiya 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Sindinakhale pansi ndi gulu la anthu okonda kuchita nthabwala+ ndi kuyamba kusangalala nawo.+ Ndakhala pansi ndekhandekha chifukwa dzanja lanu lili pa ine,+ chifukwa mwandidzaza ndi mkwiyo.+ Maliro 3:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kodi munthu angadandaulirenji+ chifukwa cha zotsatirapo za tchimo lake?+
17 Sindinakhale pansi ndi gulu la anthu okonda kuchita nthabwala+ ndi kuyamba kusangalala nawo.+ Ndakhala pansi ndekhandekha chifukwa dzanja lanu lili pa ine,+ chifukwa mwandidzaza ndi mkwiyo.+