Salimo 119:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Ndaganizira mozama za njira zanga,+Kuti mapazi anga ndiwabwezere ku zikumbutso zanu.+ Ezekieli 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu woipayo akaona+ zoipa zimene anali kuchita n’kuzisiya,+ adzakhalabe ndi moyo. Sadzafa ayi.+ Hagai 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Ganizirani mofatsa zimene mukuchita.+
28 Munthu woipayo akaona+ zoipa zimene anali kuchita n’kuzisiya,+ adzakhalabe ndi moyo. Sadzafa ayi.+