Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 19:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Zitatero, aliyense amene anaona zimenezo anati: “Zoterezi sizinachitikepo kapena kuonekapo kuchokera pa tsiku limene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo mpaka lero. Iganizireni mofatsa nkhaniyi, munenepo maganizo+ anu ndipo tigwirizane.”

  • Salimo 119:59
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  59 Ndaganizira mozama za njira zanga,+

      Kuti mapazi anga ndiwabwezere ku zikumbutso zanu.+

  • Maliro 3:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Tiyeni tifufuze njira zathu kuti tizidziwe,+ ndipo tibwerere kwa Yehova.+

  • Malaki 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mukapanda kumvera,+ ndiponso ngati simuganizira nkhani imeneyi mumtima mwanu+ kuti mulemekeze dzina langa,+ ndidzakutumizirani temberero+ ndi kutemberera madalitso anu.+ Ndatemberera dalitso la aliyense wa inu chifukwa simunaganizire nkhani imeneyi mumtima mwanu,” watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena