Levitiko 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Koma ngati simudzandimvera kapena kutsatira malamulo onsewa,+ Yesaya 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti amenewa ndi anthu opanduka,+ ana ochita zachinyengo,+ amene safuna kumva malamulo a Yehova,+
9 Pakuti amenewa ndi anthu opanduka,+ ana ochita zachinyengo,+ amene safuna kumva malamulo a Yehova,+