Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 119:101
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 101 Ndaletsa mapazi anga kuyenda m’njira iliyonse yoipa.+

      Ndachita izi kuti ndisunge mawu anu.+

  • Luka 15:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Basi ndinyamuka ndizipita+ kwa bambo anga ndikawauze kuti: “Bambo, ndachimwira kumwamba komanso ndachimwira inu.+

  • 2 Akorinto 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pitirizani kudziyesa kuti muone ngati mukadali olimba m’chikhulupiriro. Pitirizani kudziyesa kuti mudziwe kuti ndinu munthu wotani.+ Kodi simukudziwa kuti Yesu Khristu ndi wogwirizana ndi inu?+ Muyenera kudziwa zimenezi, kupatulapo ngati muli osavomerezeka.

  • Aefeso 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Choncho samalani kwambiri kuti mmene mukuyendera+ si monga anthu opanda nzeru, koma ngati anzeru.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena