Salimo 81:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu anga sanamvere mawu anga.+Ndipo Isiraeli sanasonyeze kuti ndi wofunitsitsa kundimvera.+ Yesaya 42:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Mulungu anali kuwakhuthulira mkwiyo, ukali wake, ndi nkhondo yoopsa.+ Nkhondoyo inali kuwapsereza+ koma iwo sanazindikire.+ Inapitiriza kuwatentha koma iwo sanaganizire chilichonse mumtima mwawo.+ Yesaya 57:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Kodi unachita mantha ndi ndani kuti uyambe kuopa,+ mpaka kuyamba kunama?+ Koma sunakumbukire ine.+ Palibe chimene unaganizira mumtima mwako.+ Popeza ine ndinakhala chete ndipo sindinachitepo kanthu pa zochita zako,+ iweyo sunali kundiopa.+
11 Koma anthu anga sanamvere mawu anga.+Ndipo Isiraeli sanasonyeze kuti ndi wofunitsitsa kundimvera.+
25 Choncho Mulungu anali kuwakhuthulira mkwiyo, ukali wake, ndi nkhondo yoopsa.+ Nkhondoyo inali kuwapsereza+ koma iwo sanazindikire.+ Inapitiriza kuwatentha koma iwo sanaganizire chilichonse mumtima mwawo.+
11 “Kodi unachita mantha ndi ndani kuti uyambe kuopa,+ mpaka kuyamba kunama?+ Koma sunakumbukire ine.+ Palibe chimene unaganizira mumtima mwako.+ Popeza ine ndinakhala chete ndipo sindinachitepo kanthu pa zochita zako,+ iweyo sunali kundiopa.+