Salimo 50:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Wachita zinthu zonsezi, koma ine ndinakhala chete.+Unali kuganiza kuti ine ndikhala ngati iwe.+Ine ndidzakudzudzula,+ ndipo ndidzaika machimo ako onse poyera iwe ukuona.+
21 Wachita zinthu zonsezi, koma ine ndinakhala chete.+Unali kuganiza kuti ine ndikhala ngati iwe.+Ine ndidzakudzudzula,+ ndipo ndidzaika machimo ako onse poyera iwe ukuona.+