Hoseya 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene iwo achuluka, m’pamenenso akundichimwira kwambiri.+ M’malo mondipatsa ulemu, akundinyoza.+ Hagai 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinalamula kuti chilala chigwe padziko lapansi, pamapiri, pambewu, pavinyo watsopano,+ pamafuta, pazinthu zonse zochokera munthaka, pa anthu, paziweto ndi pa ntchito iliyonse ya manja anu.’”+
11 Ndinalamula kuti chilala chigwe padziko lapansi, pamapiri, pambewu, pavinyo watsopano,+ pamafuta, pazinthu zonse zochokera munthaka, pa anthu, paziweto ndi pa ntchito iliyonse ya manja anu.’”+