Amosi 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu inu mukugona pamipando ya minyanga ya njovu+ ndi kudziwongola pamabedi, ndiponso mukudya nyama ya ana a nkhosa ndi ana amphongo onenepa a ng’ombe zanu.+ Amosi 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+ ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamabedi lidzatha.
4 Anthu inu mukugona pamipando ya minyanga ya njovu+ ndi kudziwongola pamabedi, ndiponso mukudya nyama ya ana a nkhosa ndi ana amphongo onenepa a ng’ombe zanu.+
7 “Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+ ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamabedi lidzatha.