Genesis 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Yehova anavumbitsa sulufule ndi moto kuchokera kwa Yehova kumwamba, kuvumbira pa Sodomu ndi Gomora.+ Ezekieli 16:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pali ine Mulungu wamoyo, m’bale wako Sodomu ndi midzi yake yozungulira, sanachite mofanana ndi zimene iwe ndi midzi yako yozungulira munachita,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
24 Ndiyeno Yehova anavumbitsa sulufule ndi moto kuchokera kwa Yehova kumwamba, kuvumbira pa Sodomu ndi Gomora.+
48 Pali ine Mulungu wamoyo, m’bale wako Sodomu ndi midzi yake yozungulira, sanachite mofanana ndi zimene iwe ndi midzi yako yozungulira munachita,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.