Yeremiya 52:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+ Ezekieli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uzidzadya chakudya chochita kuyeza. Tsiku lililonse uzidzadya chokwana masekeli* 20.+ Uzidzadya chakudyachi mwa apo ndi apo.
6 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+
10 Uzidzadya chakudya chochita kuyeza. Tsiku lililonse uzidzadya chokwana masekeli* 20.+ Uzidzadya chakudyachi mwa apo ndi apo.