Ezekieli 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mitengo yonse yamthengo idzadziwa kuti ine Yehova+ ndatsitsa mtengo waukulu+ ndi kukweza mtengo wonyozeka,+ ndaumitsa mtengo wauwisi+ ndi kuchititsa maluwa mtengo umene unali wouma. Ine Yehova ndanena ndi kuchita zimenezi.”’”+ Luka 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti ngati akuchita izi pamene mtengo uli wauwisi, kuli bwanji mtengowo ukadzauma?”+
24 Mitengo yonse yamthengo idzadziwa kuti ine Yehova+ ndatsitsa mtengo waukulu+ ndi kukweza mtengo wonyozeka,+ ndaumitsa mtengo wauwisi+ ndi kuchititsa maluwa mtengo umene unali wouma. Ine Yehova ndanena ndi kuchita zimenezi.”’”+