Ezekieli 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi mtima wako udzapitiriza kupirira,+ kapena kodi manja ako adzakhala ndi mphamvu m’masiku amene ndidzakulange?+ Ine Yehova ndanena ndipo ndidzachitapo kanthu.+ Ezekieli 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsoka lako lidzabwera ndithu+ ndipo ndidzachitapo kanthu. Sindidzazengereza,+ kumva chisoni+ kapena kusintha maganizo.+ Iwo adzakuweruza mogwirizana ndi njira zako ndi zochita zako.+ Ine Yehova ndanena,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
14 Kodi mtima wako udzapitiriza kupirira,+ kapena kodi manja ako adzakhala ndi mphamvu m’masiku amene ndidzakulange?+ Ine Yehova ndanena ndipo ndidzachitapo kanthu.+
14 Tsoka lako lidzabwera ndithu+ ndipo ndidzachitapo kanthu. Sindidzazengereza,+ kumva chisoni+ kapena kusintha maganizo.+ Iwo adzakuweruza mogwirizana ndi njira zako ndi zochita zako.+ Ine Yehova ndanena,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”