Yobu 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kapena kodi uli ndi dzanja ngati la Mulungu woona?+Kodi ungachititse mabingu kugunda ndi mawu ngati a Mulungu?+ 1 Akorinto 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kapena “kodi tikufuna kuputa nsanje+ ya Yehova”? Kodi mphamvu zathu zingafanane ndi zake?+
9 Kapena kodi uli ndi dzanja ngati la Mulungu woona?+Kodi ungachititse mabingu kugunda ndi mawu ngati a Mulungu?+