Yesaya 66:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Iwo adzapita kukaona mitembo ya anthu amene anali kuphwanya malamulo anga,+ pakuti mphutsi zodya mitemboyo sizidzafa. Moto woinyeketsa sudzazima+ ndipo idzakhala chinthu chonyansa kwa anthu onse.”+ Mateyu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.”
24 “Iwo adzapita kukaona mitembo ya anthu amene anali kuphwanya malamulo anga,+ pakuti mphutsi zodya mitemboyo sizidzafa. Moto woinyeketsa sudzazima+ ndipo idzakhala chinthu chonyansa kwa anthu onse.”+
12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.”