Ezekieli 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘“Koma amene akuumirira mafano awo onyansa ndi zinthu zawo zonyansa,+ ndidzawabwezera monga mwa njira zawo,” watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”+ Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+ Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
21 “‘“Koma amene akuumirira mafano awo onyansa ndi zinthu zawo zonyansa,+ ndidzawabwezera monga mwa njira zawo,” watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”+