5 popeza mayi wawo wachita dama.+ Mayi amene anatenga pakati kuti awabereke wachita zinthu zochititsa manyazi+ ndipo wanena kuti, ‘Ndikufuna kutsatira amene anali kundikonda kwambiri+ ndiponso amene anali kundipatsa chakudya, madzi, zovala za ubweya wa nkhosa, nsalu, mafuta ndi zakumwa.’+