Yeremiya 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipotu kuyambira pamene tinasiya kupereka nsembe zautsi ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa ‘mfumukazi yakumwamba,’+ chilichonse chikutisowa, ndipo tawonongeka chifukwa cha lupanga ndi njala yaikulu.+
18 Ndipotu kuyambira pamene tinasiya kupereka nsembe zautsi ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa ‘mfumukazi yakumwamba,’+ chilichonse chikutisowa, ndipo tawonongeka chifukwa cha lupanga ndi njala yaikulu.+