Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 47:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Abambo adzathawa osayang’ana m’mbuyo kuti apulumutse ana awo. Adzachita izi chifukwa chakuti sadzalimba mtima pakumva mgugu wa mahatchi ake,+ phokoso la magaleta ake ankhondo+ ndi kulira kwa mawilo ake.+

  • Ezekieli 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Fumbi limene chikhamu cha mahatchi ake chidzachite lidzakufotsera.+ Mpanda wako udzagwedezeka chifukwa cha phokoso la asilikali a pamahatchi ndi mawilo a magaleta ankhondo. Izi zidzachitika iye akamadzalowa m’zipata zako ngati mmene zimakhalira polowa mumzinda umene mpanda wake augumula.

  • Nahumu 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kukumveka kulira kwa mkwapulo,+ kulira kwa mawilo, mgugu wa mahatchi* ndi kudumpha kwa magaleta.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena