Yeremiya 47:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Abambo adzathawa osayang’ana m’mbuyo kuti apulumutse ana awo. Adzachita izi chifukwa chakuti sadzalimba mtima pakumva mgugu wa mahatchi ake,+ phokoso la magaleta ake ankhondo+ ndi kulira kwa mawilo ake.+ Ezekieli 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitunduyo idzagwetsa mpanda wa Turo+ ndi kugumula nsanja zake.+ Ine ndidzapala fumbi lake n’kumusandutsa malo osalala opanda kanthu kalikonse, apathanthwe.
3 Abambo adzathawa osayang’ana m’mbuyo kuti apulumutse ana awo. Adzachita izi chifukwa chakuti sadzalimba mtima pakumva mgugu wa mahatchi ake,+ phokoso la magaleta ake ankhondo+ ndi kulira kwa mawilo ake.+
4 Mitunduyo idzagwetsa mpanda wa Turo+ ndi kugumula nsanja zake.+ Ine ndidzapala fumbi lake n’kumusandutsa malo osalala opanda kanthu kalikonse, apathanthwe.