Yesaya 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu watambasulira dzanja lake panyanja. Wagwedeza maufumu.+ Yehova walamula kuti malo achitetezo a ku Foinike awonongedwe.+ Amosi 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzatumiza moto pakhoma la Turo ndipo udzanyeketsa nsanja zake zokhalamo.’+
11 Mulungu watambasulira dzanja lake panyanja. Wagwedeza maufumu.+ Yehova walamula kuti malo achitetezo a ku Foinike awonongedwe.+