2 Samueli 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Davide anali kukwezeka zitunda za phiri la Maolivi+ akulira, ataphimba kumutu kwake.+ Anali kuyenda wosavala nsapato ndipo aliyense mwa anthu amene anali naye anaphimba kumutu kwake ndipo onse anali kuyenda akulira.+
30 Davide anali kukwezeka zitunda za phiri la Maolivi+ akulira, ataphimba kumutu kwake.+ Anali kuyenda wosavala nsapato ndipo aliyense mwa anthu amene anali naye anaphimba kumutu kwake ndipo onse anali kuyenda akulira.+