Esitere 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zimenezi zitachitika, Moredekai anabwerera kuchipata cha mfumu.+ Koma Hamani anapita kunyumba kwake mofulumira, akulira ndiponso ataphimba kumutu.+ Yeremiya 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu otchuka atuma anthu wamba kukatunga madzi.+ Anthu wambawo afika kuzitsime koma sanapeze madzi.+ Abwerera ndi ziwiya zopanda kanthu. Achita manyazi+ ndipo akhumudwa moti aphimba mitu yawo.+
12 Zimenezi zitachitika, Moredekai anabwerera kuchipata cha mfumu.+ Koma Hamani anapita kunyumba kwake mofulumira, akulira ndiponso ataphimba kumutu.+
3 Anthu otchuka atuma anthu wamba kukatunga madzi.+ Anthu wambawo afika kuzitsime koma sanapeze madzi.+ Abwerera ndi ziwiya zopanda kanthu. Achita manyazi+ ndipo akhumudwa moti aphimba mitu yawo.+