Esitere 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’masiku amenewo, pamene Moredekai anali kukhala pansi kuchipata cha mfumu, Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri za panyumba ya mfumu, amenenso anali alonda a pakhomo, anakwiya ndipo anafuna kupha+ Mfumu Ahasiwero. Salimo 131:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 131 Inu Yehova, mtima wanga sunadzikweze,+Maso anga si onyada.+Sindinafune zinthu zapamwamba kwambiri,+Kapena zinthu zodabwitsa kwambiri.+
21 M’masiku amenewo, pamene Moredekai anali kukhala pansi kuchipata cha mfumu, Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri za panyumba ya mfumu, amenenso anali alonda a pakhomo, anakwiya ndipo anafuna kupha+ Mfumu Ahasiwero.
131 Inu Yehova, mtima wanga sunadzikweze,+Maso anga si onyada.+Sindinafune zinthu zapamwamba kwambiri,+Kapena zinthu zodabwitsa kwambiri.+