Ezekieli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Iwe mwana wa munthu, kodi anthu opanduka a nyumba ya Isiraeli+ sanakufunse kuti, ‘Kodi ukuchita chiyani?’ Ezekieli 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu a mtundu wako akayamba kukufunsa kuti, ‘Kodi sutiuza kuti zinthu izi zikutanthauza chiyani?’+
9 “Iwe mwana wa munthu, kodi anthu opanduka a nyumba ya Isiraeli+ sanakufunse kuti, ‘Kodi ukuchita chiyani?’
18 Anthu a mtundu wako akayamba kukufunsa kuti, ‘Kodi sutiuza kuti zinthu izi zikutanthauza chiyani?’+