23 Iwo adzagwira uta ndi nthungo.+ Umenewu ndi mtundu wankhanza ndipo sudzachita chisoni. Mawu awo adzamveka ngati mkokomo wa nyanja+ ndipo adzabwera pamahatchi.+ Mtunduwo wafola pokonzekera kumenya nawe nkhondo ngati mmene mwamuna wankhondo amachitira, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni.”+