Ezekieli 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitunduyo idzagwetsa mpanda wa Turo+ ndi kugumula nsanja zake.+ Ine ndidzapala fumbi lake n’kumusandutsa malo osalala opanda kanthu kalikonse, apathanthwe.
4 Mitunduyo idzagwetsa mpanda wa Turo+ ndi kugumula nsanja zake.+ Ine ndidzapala fumbi lake n’kumusandutsa malo osalala opanda kanthu kalikonse, apathanthwe.