Genesis 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ana a Semu anali Elamu,+ Ashuri,+ Aripakisadi,+ Ludi ndi Aramu. 1 Mbiri 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana a Semu+ anali Elamu,+ Ashuri,+ Aripakisadi,+ Ludi,+ Aramu,Uzi, Huli, Geteri, ndi Masi.+