Ezara 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuchokera kwa Rehumu+ mtsogoleri wa akulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse monga oweruza ndi abwanamkubwa aang’ono a kutsidya lina la Mtsinje,*+ alembi+ ena, anthu a ku Ereke,+ Ababulo,+ anthu okhala ku Susa,+ kapena kuti Aelamu,+ Machitidwe 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakati pathu pali Apati, Amedi,+ ndi Aelamu.+ Palinso anthu ochokera ku Mesopotamiya, ku Yudeya,+ ku Kapadokiya,+ ku Ponto+ ndi kuchigawo cha Asia.+
9 Kuchokera kwa Rehumu+ mtsogoleri wa akulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse monga oweruza ndi abwanamkubwa aang’ono a kutsidya lina la Mtsinje,*+ alembi+ ena, anthu a ku Ereke,+ Ababulo,+ anthu okhala ku Susa,+ kapena kuti Aelamu,+
9 Pakati pathu pali Apati, Amedi,+ ndi Aelamu.+ Palinso anthu ochokera ku Mesopotamiya, ku Yudeya,+ ku Kapadokiya,+ ku Ponto+ ndi kuchigawo cha Asia.+