Ezara 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno mfumuyo inatumiza mawu kwa Rehumu+ mtsogoleri wa akulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse+ amene anali kukhala ku Samariya, ndi kwa ena onse okhala kutsidya lina la Mtsinje. Mawuwo anali akuti: “Moni!+ Ezara 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mawu amene analembedwa m’kalata ya mfumu Aritasasita atawerengedwa pamaso pa Rehumu,+ Simusai+ mlembi, ndi anzawo,+ iwo anapita msangamsanga kwa Ayuda ku Yerusalemu n’kukawaletsa ntchitoyo mwankhondo.+
17 Ndiyeno mfumuyo inatumiza mawu kwa Rehumu+ mtsogoleri wa akulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse+ amene anali kukhala ku Samariya, ndi kwa ena onse okhala kutsidya lina la Mtsinje. Mawuwo anali akuti: “Moni!+
23 Mawu amene analembedwa m’kalata ya mfumu Aritasasita atawerengedwa pamaso pa Rehumu,+ Simusai+ mlembi, ndi anzawo,+ iwo anapita msangamsanga kwa Ayuda ku Yerusalemu n’kukawaletsa ntchitoyo mwankhondo.+