Ezara 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuchokera kwa Rehumu+ mtsogoleri wa akulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse monga oweruza ndi abwanamkubwa aang’ono a kutsidya lina la Mtsinje,*+ alembi+ ena, anthu a ku Ereke,+ Ababulo,+ anthu okhala ku Susa,+ kapena kuti Aelamu,+
9 Kuchokera kwa Rehumu+ mtsogoleri wa akulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse monga oweruza ndi abwanamkubwa aang’ono a kutsidya lina la Mtsinje,*+ alembi+ ena, anthu a ku Ereke,+ Ababulo,+ anthu okhala ku Susa,+ kapena kuti Aelamu,+