Genesis 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ana a Semu anali Elamu,+ Ashuri,+ Aripakisadi,+ Ludi ndi Aramu. Yesaya 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 M’tsiku limenelo, Yehova adzaperekanso dzanja lake kachiwiri+ kuti atenge anthu ake otsala kuchokera ku Asuri,+ ku Iguputo,+ ku Patirosi,+ ku Kusi,+ ku Elamu,+ ku Sinara,+ ku Hamati ndi m’zilumba za m’nyanja.+ Yeremiya 49:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthu a ku Elamu ndidzawabweretsera mphepo zinayi kuchokera kumalekezero anayi a kumwamba.+ Ndidzawabalalitsira kumphepo zonsezi+ ndipo sipadzapezeka mtundu wa anthu kumene obalalitsidwa+ a Elamu sadzapitako.’”
11 M’tsiku limenelo, Yehova adzaperekanso dzanja lake kachiwiri+ kuti atenge anthu ake otsala kuchokera ku Asuri,+ ku Iguputo,+ ku Patirosi,+ ku Kusi,+ ku Elamu,+ ku Sinara,+ ku Hamati ndi m’zilumba za m’nyanja.+
36 Anthu a ku Elamu ndidzawabweretsera mphepo zinayi kuchokera kumalekezero anayi a kumwamba.+ Ndidzawabalalitsira kumphepo zonsezi+ ndipo sipadzapezeka mtundu wa anthu kumene obalalitsidwa+ a Elamu sadzapitako.’”