1Awa ndi mawu a Nehemiya+ mwana wa Hakaliya. M’mwezi wa Kisilevi,*+ m’chaka cha 20,+ ine ndinali kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.+
2 Nditayamba kuona masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani,+ imene ili m’chigawo cha Elamu.+ M’masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili m’mphepete mwa mtsinje wa Ulai.+